Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Solomo anaimirira ku guwa la nsembe la Yehova pamaso pa msonkhano wonse wa Israyeli, natambasulira manja ace kumwamba, nati,

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:22 nkhani