Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 7:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamanga khumbi la nsanamira, m'litali mwace munali mikono makumi asanu, kupingasa kwace mikono makumi atatu; ndipo panali khumbi lina patsogolo pace, ndi nsanamira ndi mitanda patsogolo pacepo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:6 nkhani