Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 7:51 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Motero nchito zonse zinatsirizika, zimene mfumu Solomo anacitira nyumba ya Yehova. Ndipo Solomo analonga zinthu adazipatula Davide atate wace, ndizo siliva ndi golidi ndi zipangizo zomwe naziika mosungira cuma ca nyumba ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:51 nkhani