Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 7:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pa matsekerezo a pakati pa mbano panali ngati mikango ndi ng'ombe ndi akerubi, ndi pamwamba pa mbano panali cosanjikirapo; ndipo pansi pa mikango ndi ng'ombe panaphatikizika zotsetseremba zoyangayanga zokoloweka.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:29 nkhani