Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 7:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anamanganso nyumba yochedwa Nkhalango ya Lebano, m'litali mwace munali mikono zana limodzi, kupingasa kwace mikono makumi asanu, ndi msinkhu wace mikono makumi atatu; naisanja pa mizere inai ya mapanda amkungudza, ndi mitanda yamkungudza yotanthalika mapandawo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:2 nkhani