Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 6:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'caka cakhumi ndi cimodzi m'mwezi wa Buli ndiwo mwezi wacisanu ndi citatu anatsiriza nyumba konse konse monga mwa mamangidwe ace onse. Momwemo anaimanga zaka zisanu ndi ziwiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 6

Onani 1 Mafumu 6:38 nkhani