Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 5:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akapolo anga adzatsika nayo ku Lebano kufika nayo ku nyanja yamcere, ndipo ine ndidzaiyandamitsa paphaka kufikira komwe mudzandiuzako, ndi kumeneko ndidzaimasula, ndipo mudzaitenga; nimudzacita cifuniro canga, kumapatsa banja langa zakudya.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 5

Onani 1 Mafumu 5:9 nkhani