Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 5:17-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Ndipo mfumu inalamula iwo, natuta miyala yaikuru-ikuru ya mtengo wapatali, kuika maziko ace a nyumbayo ndi miyala yosemasema.

18. Ndipo omanga nyumba a Solomo ndi omanga nyumba a Hiramu ndi anthu a ku Gebala anaisema, naikonza mitengo ndi miyala yakumangira nyumbayo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 5