Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 5:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anawatuma ku Lebano mwezi umodzi zikwi khumi kuwasintha, mwezi umodzi iwo anali ku Lebano, miyezi iwiri anali kwao; ndipo Adoniramu anali kapitao wa athangata.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 5

Onani 1 Mafumu 5:14 nkhani