Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 4:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akapitao aja anatengetsera cakudya Solomo ndi anthu onse akudya ku gome la mfumu Solomo, munthu yense m'mwezi mwace, sanalola kanthu kasoweke.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 4

Onani 1 Mafumu 4:27 nkhani