Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 4:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ayuda ndi Aisrayeli anakhala mosatekeseka, munthu yense patsinde pa mpesa wace ndi mkuyu wace, kuyambira ku Dani mpaka ku Beeriseba, masiku onse a Solomo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 4

Onani 1 Mafumu 4:25 nkhani