Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 4:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo mfumu Solomo anali mfumu ya Israyeli yense.

2. Ndipo akuru a mfumu ndi awa: Azariya mwana wa Zadoki anali nduna,

3. Elihorepa ndi Ahiya ana a Sisa alembi, Yehosafati mwana wa Ahiludi wolembera mbiri,

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 4