Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 3:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Patsani tsono kapolo wanu mtima womvera wakuweruza anthu anu; kuti ndizindikire pakati pa zabwino ndi zoipa; pakuti akutha ndani kuweruza anthu anu ambiri amene?

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:9 nkhani