Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 3:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inapita ku Gibeoni kukaphera nsembe kumeneko; popeza msanje waukuru unali kumeneko, Solomo anapereka nsembe zopsereza cikwi cimodzi pa guwalo la nsembe.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:4 nkhani