Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 3:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mkazi amene mwana wamoyo anali wace analankhula ndi mfumu, popeza mtima wace unalira mwana wace, nati, Ha! mbuye wanga, mumpatse uyo mwana wamoyo osamupha konse. Koma winayo anati, Asakhale wanga kapena wako, dulani.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:26 nkhani