Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 3:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunacitika kuti tsiku lacitatu nditaona ine mwana, mnzangayu anaonanso mwana; ndipo ife tinali pamodzi, munalibe mlendo ndi ife m'nyumbamo, koma ife awiri m'nyumbamo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:18 nkhani