Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 3:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu anati kwa iye, Popeza wapempha cimeneci, osadzipemphera masiku ambiri, osadzipempheranso cuma, osadzipempheranso moyo wa adani ako, koma wadzipemphera nzeru zakumvera mirandu;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:11 nkhani