Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 22:52-53 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

52. Nacita coipa pamaso pa Yehova, nayenda m'njira ya atate wace, ndi ya amace, ndi ya Yerobiamu mwana wa Nebati, amene adacimwitsa Israyeli.

53. Natumikira Baala, namweramira, naputa mkwiyo wa Yehova Mulungu wa Israyeli, monga umo anacitira atate wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22