Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 22:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehosafati anali wa zaka makumi atatu mphambu zisanu, pamene analowa ufumu, nakhala nifumu zaka makumi awiri mphambu zisanu m'Yerusalemu. Ndi dzina la amace linali Azuba mwana wa Sili.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22

Onani 1 Mafumu 22:42 nkhani