Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 22:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono anati kwa Yehosafati, Kodi udzapita nane kunkhondo ku Ramoti Gileadi? Ndipo Yehosafati anati kwa mfumu ya Israyeli, M'mene ukhalira iwe ndi momwe ndikhalira ndine; anthu anga monga anthu ako, akavalo anga monga akavale ako.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22

Onani 1 Mafumu 22:4 nkhani