Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 22:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo potsuka garetayo pa thawale la ku Samaria agaru ananyambita mwazi wace, pala pamasamba akazi adama, monga mwa mau a Yehova amene ananenawo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22

Onani 1 Mafumu 22:38 nkhani