Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 22:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano taonani, Yehova waika mzimu wonama m'kamwa mwa aneneri anu onse awa, ndipo Yehova ananena coipa ca inu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22

Onani 1 Mafumu 22:23 nkhani