Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 22:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono mthenga uja udakaitana Mikaya unanena naye, nati, Taona, mau a aneneri abvomerezana zokoma kwa mfumu ndi m'kamwa m'modzi; mau ako tsono afanane ndi mau a wina wa iwowo, nunene zabwino.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22

Onani 1 Mafumu 22:13 nkhani