Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 22:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu ya Israyeli ndi Yehosafati mfumu ya Yuda anakhala onse awiri, yense pa mpando wacifumu wace, obvala zobvala zao zacifumu pabwalo pa khomo la cipata ca Samaria; ndipo aneneri onse ananenera pamaso pao.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22

Onani 1 Mafumu 22:10 nkhani