Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 21:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ahabu analowa m'nyumba mwace wamsunamo ndi wokwiya, cifukwa ca mau amene Naboti wa ku Yezreeli adalankhula naye; popeza adati, Sindikupatsani colowa ca makolo anga. M'mwemo anagona pa kama wace, nayang'ana kumbali, nakana kudya mkate.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 21

Onani 1 Mafumu 21:4 nkhani