Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 21:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ahabu anati kwa Eliya, Wandipeza kodi, mdani wangawe? Nayankha, Ndakupeza; pokhala wadzigulitsa kucita coipaco pamaso pa Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 21

Onani 1 Mafumu 21:20 nkhani