Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 21:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nyamuka, tsikira kukakomana ndi Ahabu mfumu ya Israyeli, akhala m'Samariya; taona, ali ku munda wamphesa wa Naboti kumene anatsikira kukaulandira.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 21

Onani 1 Mafumu 21:18 nkhani