Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 21:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu aja a mudzi wace, ndiwo akulu ndi omveka adakhala m'mudzi mwace, anacita monga Yezebeli anawatumizira, monga munalembedwa m'akalata amene iye anawatumizira.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 21

Onani 1 Mafumu 21:11 nkhani