Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 20:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo popitapa mfumu, anapfuula kwa mfumu, nati, Kapolo wanu analowa pakati pa nkhondo, ndipo taonani, munthu anapambuka nabwera ndi munthu kwa ine, nati, Tasunga munthu uyu; akasowa ndi cifukwa ciri conse moyo wako udzakhala m'malo mwa moyo wace, kapena udzalipa talenti la siliva.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 20

Onani 1 Mafumu 20:39 nkhani