Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 20:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Benihadadi anati kwa iye, Ndidzabweza midzi ija atate wanga analanda kwa atate wanu; ndipo mudzikonzere mabwalo a malonda m'Damasiko, monga umo atate wanga anadzikonzera m'Samaria. Ndi ine, ati Ahabu, ndikulola umuke ndi pangano ili. Tsono anapangana naye, namlola amuke.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 20

Onani 1 Mafumu 20:34 nkhani