Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 20:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo amenewo anaturuka usana. Koma Benihadadi analinkumwa naledzera m'misasamo, iye ndi mafumu aja makumi atatu mphambu awiri aja akumthandiza.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 20

Onani 1 Mafumu 20:16 nkhani