Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 20:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunacitika, atamva Benihadadi mau awa, analikumwa nao mafumu m'misasa, ananena ndi anyamata ace, Nikani. Nandandalika pamudzipo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 20

Onani 1 Mafumu 20:12 nkhani