Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 2:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso udziwa cimene Yoabu mwana wa Zeruya anandicitira, inde cimene anawacitira akazembe awiri aja a magulu a nkhondo a Israyeli, ndiwo Abineri mwana wa Neri, ndi Amasa mwana wa Yeteri, amene aja anawapha, nakhetsa mwazi ngati wa nkhondo masiku a mtendere, napaka mwazi wa nkhondo pa lamba lace la m'cuuno mwace, ndi pa nsapato za pa mapazi ace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2

Onani 1 Mafumu 2:5 nkhani