Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 2:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono mfumu inanenanso ndi Simeyi, Udziwa iwe coipa conse mtima wako umadziwaco, cimene udacitira Davide atate wanga; cifukwa cace Yehova adzakubwezera coipa cako pamutu pako mwini.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2

Onani 1 Mafumu 2:44 nkhani