Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 2:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inatuma munthu kukaitana Simeyi, niti kwa iye, Kodi sindinakulumbiritsa pa Yehova ndi kukucenjeza, kuti, Tadziwa ndithu, kuti tsiku lakuturuka iwe ndi kukayenda kwina konse udzafa ndithu? Ndipo iwe unati kwa ine, Mau amene ndawamva ndi abwino.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2

Onani 1 Mafumu 2:42 nkhani