Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 2:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova adzambwezera mwazi wace pa mutu wace wa iye yekha, popeza iye anawakantha anthu awiri olungama ndi okoma oposa iye mwini, nawapha ndi lupanga, atate wanga Davide osadziwa, ndiwo Abineri mwana wa Neri kazembe wa khamu la nkhondo la Israyeli, ndi Amasa mwana wa Yeteri kazembe wa khamu la nkhondo la Yuda.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2

Onani 1 Mafumu 2:32 nkhani