Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 2:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nusunge cilangizo ca Yehova Mulungu wako, kuyenda m'njira zace, kusunga malemba ndi malamulo ndi maweruzo ndi umboni wace, monga mulembedwa m'cilamulo ca Mose, kuti ukacite mwa nzeru m'zonse ukacitazo, ndi kumene konse ukatembenukirako;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2

Onani 1 Mafumu 2:3 nkhani