Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 2:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu Solomo anayankha, nati kwa amai wace, Mupempheranji Abisagi wa ku Sunamu akhale wace wa Adoniya? Mumpempherenso ufumu, popeza ndiye mkuru wanga; inde ukhale wace, ndi wa Abyatara wansembeyo, ndi wa Yoabu mwana wa Zeruya.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2

Onani 1 Mafumu 2:22 nkhani