Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 19:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono anauka, nadya namwa, nayenda ndi mphamvuya cakudya cimeneco masiku makumi anai usana ndi usiku, nafika ku phiri la Mulungu ku Horebu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 19

Onani 1 Mafumu 19:8 nkhani