Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 19:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iye mwini analowa m'cipululu ulendo wa tsiku limodzi, nakakhala pansi patsinde pa mtengo watsanya, napempha kuti afe; nati, Kwafikira, cotsani tsopano moyo wanga, Yehova; popeza sindiri wokoma woposa makolo anga.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 19

Onani 1 Mafumu 19:4 nkhani