Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 18:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Obadiya ali m'njira, taona, Eliya anakomana naye; iye namdziwa, namgwadira, nati, Ndinu kodi mbuye wanga Eliya?

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:7 nkhani