Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 18:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eliya anati kwa iwo, Gwirani aneneri a Baala, asapulumuke ndi mmodzi yense. Nawagwira, ndipo Eliya ana pita nao ku mtsinje wa Kisoni, nawapha pamenepo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:40 nkhani