Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 18:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, litapendeka dzuwa, ananenera kufikira nthawi ya kupereka nsembe; koma panalibe mau, kapena wobvomereza, kapena wakuwamvera.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:29 nkhani