Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 18:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atipatse tsono ng'ombe ziwiri; ndipo adzisankhire iwo eni ng'ombe imodzi, naiduledule, naiike pankhuni osasonkhapo moto; ndipo ine ndidzakonza ng'ombe yinayo, ndi kulika pankhuni osasonkhapo moto.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:23 nkhani