Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 18:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eliya anayandikira kwa anthu onse, nati, Mukayika-kayika kufikira liti? ngati Yehova ndiye Mulungu, mtsateni iye; ngati Baala, mumtsate iyeyo. Ndipo anthu nnena kumyankha mau amodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:21 nkhani