Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 18:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iye, Sindimabvuta Israyeli ine ai, koma inu ndi nyumba ya atate wanu; popeza munasiya malamulo a Yehova, ndi kutsata Abaala.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:18 nkhani