Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 18:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzacitika, ine ntakusiyani, mzimu wa Yehova udzakunyamulirani kosakudziwa ine, ndipo ine ntakauza Ahabu, ndipo akalephera kukupezani, adzandipha. Koma ine kapolo wanu ndimaopa Yehova kuyambira ubwana wanga.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:12 nkhani