Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 18:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pali Yehova Mulungu wanu, ngati kuli mtundu umodzi wa anthu, kapena ufumu, kumene mbuye wanga sanatumako kukufunani, ndipo pakunena iwo, Palibe iye, analumbiritsa ufumu umene ndi mtundu umene kuti sanakupezani.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:10 nkhani