Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 17:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mkazi anati kwa Eliya, Ndizindikira tsopano kuti ndinu munthu wa Mulungu, ndi kuti mau a Yehova ali m'kamwa mwanuwo ngoona.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 17

Onani 1 Mafumu 17:24 nkhani