Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 16:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso mau a Yehova anadza ndi dzanja la mneneri Yehu mwana wa Hanani, kutsutsa Basa ndi nyumba yace, cifukwa ca zoipa zonse anazicita iye pamaso pa Yehova; popeza anaputa mkwiyo wace ndi macitidwe a manja ace, nafanana ndi nyumba ya Yerobiamu; ndiponso popeza anaikantha.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 16

Onani 1 Mafumu 16:7 nkhani